2 Chronicles 31:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ansembe adalembedwa pamodzi ndi ana ao onse akhanda, akazi ao, ana ao aamuna ndi aakazi, kungoti onse a m'banja mwao, chifukwa anali oyenera kudziyeretsa mokhulupirika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi iwo oyesedwa mwa chibadwidwe cha ana ao ang'ono onse, akazi ao, ndi ana ao aamuna ndi aakazi, mwa msonkhano wonse; pakuti m'kukhulupirika kwao anadzipatula akhale opatulika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anaphatikizanso ana onse aangʼono, akazi ndiponso ana aamuna ndi ana aakazi a gulu lonse amene analembedwa mʼmbiri ya mibado yawo iyi, pakuti anakhulupirika pa kudzipatula okha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi iwo oyesedwa mwa cibadwidwe ca ana ao ang'ono onse, akazi ao, ndi ana ao amuna ndi akazi, mwa msonkhano wonse; pakuti m'kukhulupirika kwao anadzipatula akhale opatulika;