2 Chronicles 31:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adalamula anthu a ku Yerusalemu kuti azipereka chigawo choyenera ansembe ndi Alevi, kuti pakutero ansembe ndi Aleviwo azidzipereka ku malamulo a Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anauzanso anthu okhala m'Yerusalemu apereke gawo la ansembe ndi Alevi, kuti iwowa alimbike m'chilamulo cha Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyo inalamula anthu amene amakhala mu Yerusalemu kupereka gawo lawo kwa ansembe ndi Alevi kuti iwowo adzipereke ku malamulo a Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anauzanso anthu okhala m'Yerusalemu apereke gawo la ansembe ndi Alevi, kuti iwowa alimbike m'cilamulo ca Yehova.