2 Chronicles 31:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adayamba kumaunjika milu pa mwezi wachitatu natsiriza pa mwezi wachisanu ndi chiŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwezi wachitatu anayamba kuika miyalo ya miyuluyi, naitsiriza mwezi wachisanu ndi chiwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anayamba kuchita izi mwezi wachitatu ndipo anatsiriza mwezi wachisanu ndi chiwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwezi wacitatu anayamba kuika miyalo ya miyuruyi, naitsiriza mwezi wacisanu ndi ciwiri.