2 Chronicles 32:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Senakeribu, mfumu ya ku Asiriya, akufunsa kuti, ‘Kodi mukukhulupirira chiyani, kuti muzikanirira mu Yerusalemu ndi kumatsekedwa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Senakeribu mfumu ya Asiriya, Mutama chiyani kuti mukhala m'linga m'Yerusalemu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Senakeribu mfumu ya ku Asiriya akuti: Kodi inu mukukhulupirira chiyani, kuti mukukhalabe mu Yerusalemu mutazingidwa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Sanakeribu mfumu ya Asuri, Mutama ciani kuti mukhala m'linga m'Yerusalemu?