2 Chronicles 32:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi Hezekiya sakukulakwitsani, kuti akuphetseni ndi njala ndi ludzu, pamene akukuuzani kuti, “Chauta, Mulungu wathu, adzatipulumutsa kwa mfumu ya ku Asiriya?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sakukopani Hezekiya, kuti akuperekeni mufe nayo njala ndi ludzu, ndi kuti, Yehova Mulungu wathu adzatilanditsa m'dzanja la mfumu ya Asiriya?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Hezekiya akunena kuti ‘Yehova Mulungu wathu adzatipulumutsa kuchoka mʼdzanja la mfumu ya ku Asiriya,’ iye akukusocheretsani, kuti mufe ndi njala ndi ludzu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sakukopani Hezekiya, kuti akuperekeni mufe nayo njala ndi ludzu, ndi kuti, Yehova Mulungu wathu adzatilanditsa m'dzanja la mfumu ya Asuri?