2 Chronicles 32:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankalankhula za Mulungu wa ku Yerusalemu monga momwe ankalankhulira za milungu ya mitundu ina ya anthu a pa dziko lapansi, imene ili milungu yopangidwa ndi manja a anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanenera Mulungu wa Yerusalemu, monga umo amanenera milungu ya mitundu ya anthu a pa dziko lapansi, ndiyo ntchito ya manja a anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayankhula za Mulungu wa Yerusalemu monga anayankhulira za milungu ya anthu ena a pa dziko lapansi, ntchito ya manja a anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanenera Mulungu wa Yerusalemu, monga umo amanenera milungu ya mitundu ya anthu a pa dziko lapansi, ndiyo nchito ya manja a anthu.