2 Chronicles 32:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Hezekiya ataona kuti Senakeribu wabwera, ndipo akufuna kuthira nkhondo Yerusalemu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakuona Hezekiya kuti wadza Senakeribu, ndi kuti nkhope yake inalunjikitsa kuyambana nkhondo ndi Yerusalemu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Hezekiya anaona kuti Senakeribu wabwera ndipo wakonzeka kuchita nkhondo ndi Yerusalemu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakuona Hezekiya kuti wadza Sanakeribu, ndi kuti nkhope yace inalunjikitsa kuyambana nkhondo ndi Yerusalemu,