2 Chronicles 32:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo mfumu Hezekiya pamodzi ndi mneneri Yesaya mwana wa Amozi, adayamba kupemphera, nafuulira kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hezekiya mfumu, ndi Yesaya mneneri mwana wa Amozi, anapemphera pa ichi, nafuulira Kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Hezekiya ndi mneneri Yesaya mwana wa Amozi anafuwulira kumwamba mʼpemphero chifukwa cha zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hezekiya mfumu, ndi Yesaya mneneri mwana wa Amozi, anapemphera pa ici, napfuulira Kumwamba.