2 Chronicles 32:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanganso nyumba zosungiramo tirigu, vinyo ndi mafuta. Adamanga makola a mitundu yonse ya ziŵeto zosiyanasiyana ndi makola a nkhosa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi nyumba zosungiramo zipatso za tirigu, ndi vinyo, ndi mafuta, ndi zipinda za nyama iliyonse, ndi makola a zoweta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anamanganso nyumba zosungiramo tirigu, vinyo watsopano ndi mafuta a olivi, ndiponso anamanga nyumba zodyeramo ngʼombe zosiyanasiyana, ndi makola a nkhosa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi nyumba zosungiramo zipatso za tirigu, ndi vinyo, ndi mafuta, ndi zipinda za nyama iri yonse, ndi makola a zoweta.