2 Chronicles 32:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso adamanga mizinda yake, ndipo anali ndi nkhosa ndi ng'ombe zambirimbiri, pakuti Mulungu adaamlemeza kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nadzimangiranso midzi, nadzionera nkhosa ndi ng'ombe zochuluka; pakuti Mulungu adampatsa chuma chambirimbiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo anamanga midzi ndipo anali ndi nkhosa ndi ngʼombe zambiri, pakuti Mulungu anamupatsa chuma chambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nadzimangiranso midzi, nadzionera nkhosa ndi ng'ombe zocuruka; pakuti Mulungu adampatsa cuma cambirimbiri.