2 Chronicles 32:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adaika atsogoleri ankhondo kuti azilamula anthu, naŵasonkhanitsa anthuwo pa bwalo ku chipata cha mzindawo. Tsono adaŵalankhula moŵalimbitsa mtima kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Naika akazembe a nkhondo alamulire anthu, nawasonkhanitsira kuli iye kubwalo la kuchipata cha mudzi, nanena nao motonthoza mtima wao ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anasankha atsogoleri a ankhondo olamulira anthu ndipo anawasonkhanitsa pamaso pake pa bwalo la chipata cha mzinda ndi kuwalimbikitsa ndi mawu awa:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naika akazembe a nkhondo alamulire anthu, nawasonkhanitsira kuli iye ku bwalo la ku cipata ca mudzi, nanena nao motonthoza mtima wao ndi kuti,