2 Chronicles 32:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Khalani amphamvu, limbani mtima. Musati muwope kapena kutaya mtima pamaso pa mfumu ya ku Asiriya ndi chigulu chankhondo chimene ali nachochi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Limbani, mulimbike mtima, musaopa kapena kutenga nkhawa pankhope pa mfumu ya Asiriya ndi aunyinji okhala naye; pakuti okhala nafe achuluka koposa okhala naye;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Khalani amphamvu ndi olimba mtima. Musachite mantha kapena kutaya mtima chifukwa cha mfumu ya ku Asiriya ndi gulu lalikulu lankhondo limene ali nalo, pakuti ife tili ndi mphamvu yayikulu kuposa imene ili ndi iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Limbani, mulimbike mtima, musaopa kapena ku tenga nkhawa pankhope pa mfumu ya Asuri ndi aunyinji okhala naye; pakuti okhala nafe acuruka koposa okhala naye;