2 Chronicles 33:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanga maguwa achikunja m'Nyumba ya Chauta imene Chauta mwini wake anali atanena kuti, “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namanga maguwa a nsembe m'nyumba ya Yehova, imene Yehova adati, M'Yerusalemu mudzakhala dzina langa kunthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Manase anamanga maguwa mʼNyumba ya Yehova, mʼmene Yehova ananena kuti, “Ine ndidzakhala mu Yerusalemu mpaka muyaya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namanga maguwa a nsembe m'nyumba ya Yehova, imene Yehova adati, M'Yerusalemu mudzakhala dzina langa ku nthawi zonse.