2 Chronicles 34:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yosiya anali wa zaka zisanu ndi zitatu pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 31 ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wake, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi atatu mphambu chimodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yosiya anali wa zaka zisanu ndi zitatu pamene anakhala mfumu, ndipo analamulira mu Yerusalemu kwa zaka 31.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi atatu mphambu cimodzi.