2 Chronicles 34:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Hilikiyayo adauza Safani mlembi kuti, “Ndalipeza buku la Malamulo lija m'Nyumba ya Chauta.” Ndipo adapereka bukulo kwa Safani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hilikiya anayankha nati kwa Safani mlembi, Ndapeza buku la chilamulo m'nyumba ya Yehova. Hilikiya napereka buku kwa Safani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hilikiya anati kwa Safani, mlembi wa zochitika, “Ine ndapeza Buku la Malamulo mʼNyumba ya Yehova.” Iye analipereka kwa Safani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Hilikiya anayankha nati kwa Safani mlembi, Ndapeza buku la cilamulo m'nyumba ya Yehova. Hilikiya napereka buku kwa Safani.