2 Chronicles 34:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Safani adadza nalo kwa mfumu, ndiponso adauza mfumu kuti, “Zonse zimene mudauza atumiki anu kuti achite, akuchita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Safani anamuka nalo buku kwa mfumu, nabwezeranso mau kwa mfumu, ndi kuti, Zonse mudazipereka kwa anyamata anu alikuzichita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Safani anapita nalo bukulo kwa mfumu ndi kumufotokozera kuti: “Akuluakulu anu akuchita zonse zimene zinapatsidwa kwa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Safani anamuka nalo buku kwa mfumu, nabwezeranso mau kwa mfumu, ndi kuti, Zonse mudazipereka kwa anyamata anu alikuzicita.