2 Chronicles 34:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhuthula ndalama zimene zinali m'Nyumba ya Chauta, azipereka kwa akapitao ndi kwa antchito.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakhuthula ndalama zinapezeka m'nyumba ya Yehova, nazipereka m'manja a akapitao ndi m'manja a antchito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo alipira ndalama zimene zinali mʼNyumba ya Yehova ndipo azipereka kwa akapitawo ndi anthu antchito.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakhuthula ndarama zinapezeka m'nyumba ya Yehova, nazipereka m'manja a akapitao ndi m'manja a anchito.