2 Chronicles 34:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo idalamula Hilikiya, Ahikamu mwana wa Safani, Abidoni mwana wa Mika, Safani mlembi uja ndi Asaya mtumiki wa mfumu kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu niuza Hilikiya, ndi Ahikamu mwana wa Safani, ndi Abidoni mwana wa Mikaya, ndi Safani mlembi, ndi Asaya mnyamata wa mfumu, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye analamula izi kwa Hilikiya, Ahikamu mwana wa Safani, Abidoni mwana wa Mika, Safani mlembi wa zochitika ndi Asaya mtumiki wa mfumu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu niuza Hilikiya, ndi Ahikamu mwana wa Safani, ndi Abidoni mwana wa Mikaya, ndi Safani mlembi, ndi Asaya mnyamata wa mfumu, ndi kuti,