2 Chronicles 34:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo adaŵauza kuti, “Chauta, Mulungu wa Israele, akunena kuti, Muuzeni munthu amene wakutumani kwa Ineyo kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye ananena nao, Atero Yehova Mulungu wa Israele, Muuze munthuyo anakutumizani kwa ine,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anati kwa anthuwo, “Yehova Mulungu wa Israeli akuti, muwuzeni munthu amene wakutumani kwa ineyo kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye ananena nao, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Muuze munthuyo anakutumizani kwa ine,