2 Chronicles 34:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine Chauta ndikuti, Ndidzabweretsa choipa ku mzinda uno ndi pa anthu onse am'menemo, potsata matemberero onse olembedwa m'buku limene adaliŵerenga pamaso pa mfumu ya ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Yehova, Taonani, ndifikitsira malo ano ndi anthu okhala m'mwemo choipa, ndicho matemberero onse olembedwa m'buku adaliwerenga pamaso pa mfumu ya Yuda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Yehova akunena kuti, Ine ndidzabweretsa mavuto pamalo pano ndi pa anthu ake, matemberero onse amene alembedwa mʼbukuli amene awerengedwa pamaso pa mfumu ya Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Yehova, Taonani, ndifikitsira malo ano ndi anthu okhala m'mwemo coipa, ndico matemberero onse olembedwa m'buku adaliwerenga pamaso pa mfumu ya Yuda;