2 Chronicles 34:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yosiya adauza anthu onse amene anali mu Yerusalemu ndi ku Benjamini kuti azisunga chipanganocho. Ndipo nzika za mu Yerusalemu zidatsatadi chipangano cha Mulungu, Mulungu wa makolo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Naimiritsapo onse okhala m'Yerusalemu ndi m'Benjamini. Ndipo okhala m'Yerusalemu anachita monga mwa chipangano cha Mulungu, Mulungu wa makolo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yosiya anawuza aliyense amene anali mu Yerusalemu ndi Benjamini kuti azisunga panganoli. Anthu a mu Yerusalemu anachita izi motsata pangano la Mulungu, Mulungu wa makolo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naimiritsapo onse okhala m'Yerusalemu ndi m'Benjamini. Ndipo okhala m'Yerusalemu anacita monga mwa cipangano ca Mulungu, Mulungu wa makolo ao.