2 Chronicles 35:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yosiya adachita Paska ku Yerusalemu, kuchitira Chauta. Adapha mwanawankhosa wa Paska pa tsiku la 14 la mwezi woyamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yosiya anachitira Yehova Paska m'Yerusalemu, naphera Paska tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi woyamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yosiya anachita chikondwerero cha Paska wa Yehova mu Yerusalemu, ndipo mwana wankhosa wa Paska anaphedwa pa tsiku la khumi ndi chinayi la mwezi woyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yosiya anacitira Yehova Paskha m'Yerusalemu, naphera Paskha tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi woyamba.