2 Chronicles 35:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adachita Paska imeneyi pa chaka cha 18 cha ufumu wa Yosiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yosiya atakhala mfumu zaka khumi ndi zisanu ndi ziwiri anachita Paska amene.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikondwerero cha Paska ichi chinachitika mʼchaka cha 18 cha ulamuliro wa Yosiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yosiya atakhala mfumu zaka khumi ndi zisanu ndi ziwiri anacita Paskha amene.