2 Chronicles 35:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaika ansembe pa maudindo ao, namaŵalimbitsa mtima pa ntchito yotumikira ku Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaika ansembe pa udikiro wao, nawalimbikitsa achite utumiki wa nyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anasankha ansembe pa maudindo awo ndipo anawalimbikitsa pa ntchito ya mʼnyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaika ansembe pa udikiro wao, nawalimbikitsa acite utumiki wa nyumba ya Yehova.