2 Chronicles 35:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo anthu oponya mivi adamlasa mfumu Yosiya. Apo mfumuyo idauza anyamata ake kuti, “Chotseni, poti ndalasidwa koipa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo oponya anayang'anitsa mivi pa mfumu Yosiya, niti mfumu kwa anyamata ake, Ndichotseni ndalasidwa ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu oponya mivi analasa mfumu Yosiya, ndipo iye anawuza akuluakulu ake, “Chotseni. Ndavulazidwa kwambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo oponya anayang'anitsa mibvi pa mfumu Yosiya, niti mfumu kwa anyamata ace, Ndicotseni ndalasidwa ndithu.