2 Chronicles 35:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ntchito zina zonse za Yosiya ndi ntchito zake zabwino zimene adazichita, potsata zimene zidalembedwa m'malamulo a Chauta,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Machitidwe ena tsono a Yosiya, ndi ntchito zake zokoma, monga mulembedwa m'chilamulo cha Yehova,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zochitika zina za ulamuliro wa Yosiya ndi ntchito za kudzipereka kwake, monga zinalembedwa mʼMalamulo a Yehova,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Macitidwe ena tsono a Yosiya, ndi nchito zace zokoma, monga mulembedwa m'cilamulo ca Yehova,