2 Chronicles 35:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mugaŵikane m'magulu malinga ndi mabanja anu, potsata zimene adalemba Davide mfumu ya Israele ndi zimene adalemba Solomoni mwana wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzikonzere monga mwa nyumba za makolo anu, m'zigawo zanu, monga umo adalembera Davide mfumu ya Israele, ndi umo adalembera Solomoni mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukhale mʼmagulu anu molingana ndi mabanja anu, molingana ndi momwe analembera Davide mfumu ya Israeli ndiponso mwana wake Solomoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzikonzere monga mwa nyumba za makolo anu, m'zigawo zanu, monga umo adalembera Davide mfumu ya Israyeli, ndi umo adalembera Solomo mwana wace.