2 Chronicles 35:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muziimirira ku malo opatulika potsata magulu a mabanja a abale anu amene sali ansembe. Ndipo banja lililonse la Alevi likhale ndi chigawo chake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muimirire m'malo opatulika, monga mwa magawidwe a nyumba za makolo za abale anu ana a anthu, akhale nalo onse gawo la nyumba ya makolo ya Alevi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Muziyima ku malo opatulika pamodzi ndi gulu la Alevi oyimira gulu lililonse lalingʼono la mabanja a abale anu amene ndi anthu wamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muimirire m'malo opatulika, monga mwa magawidwe a nyumba za makolo za abale anu ana a anthu, akhale nalo onse gawo la nyumba ya makolo ya Alevi.