2 Chronicles 36:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nebukadinezara, mfumu ya ku Babiloni, adabwera kudzamenyana naye nkhondo. Adammanga maunyolo kunka naye ku Babiloni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni anakwera kuyambana naye, nammanga ndi matangadza kumuka naye ku Babiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nebukadinezara, mfumu ya ku Babuloni anachita naye nkhondo ndipo anamumanga ndi zingwe zamkuwa ndi kumutenga kupita naye ku Babuloni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anakwera kuyambana naye, nammanga ndi matangadza kumuka naye ku Babulo.