2 Chronicles 4:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Solomoni adapanga guwa lamkuŵa, m'litali mwake mamita asanu ndi anai, m'mimba mwake asanu ndi anainso, ndipo msinkhu wake pafupi mamita anai ndi theka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapanganso guwa la nsembe lamkuwa, m'litali mwake mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwake mikono makumi awiri, ndi msinkhu wake mikono khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Solomoni anapanga guwa lamkuwa limene mulitali mwake linali mamita asanu ndi anayi, mulifupi mwakenso mamita asanu ndi anayi ndipo msinkhu wake unali mamita anayi ndi theka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapanganso guwa la nsembe lamkuwa, m'litali mwace mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace mikono khumi.