2 Chronicles 4:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adaika thanki lija pa ndonyo yakumwera ya Nyumbayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaika thawalelo ku dzanja lamanja la nyumba kum'mawa chakumwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anayika mbiya ija mbali yakummwera pamene mbali ya kummawa ndi kummwera zimakumana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaika thawalelo ku dzanja lamanja la nyumba kum'mawa cakumwela.