2 Chronicles 4:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiye kuti kumanga nsanamira ziŵiri zija, kupanga makapotolosi aŵiri aja okhala pamwamba pa nsanamirazo, ndiponso maukonde aŵiri aja ophimba ziwaya ziŵiri zija za kunsonga kwa makapotolosi aja okhala pamwamba pa nsanamira. Adapanganso maukonde aŵiri ovundikira pamwamba pa mbale ziŵiri za pa mitu imene inali pamwamba pa nsanamira ija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nsanamira ziwiri, ndi zikhozo, ndi mitu iwiri inali pamwamba pa nsanamirazo, ndi maukonde awiri akukuta zikho ziwiri za mitu ili pamwamba pa nsanamirazo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nsanamira ziwiri; mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo; maukonde awiri okongoletsera mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nsanamira ziwiri, ndi zikhozo, ndi mitu iwiri inali pamwamba pa nsanamirazo, ndi maukonde awiri akukuta zikho ziwiri za mitu iri pamwamba pa nsanamirazo,