2 Chronicles 4:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatsirizanso kupanga makangaza 400 amaukonde aŵiri aja, mizere iŵiri ya makangaza pa ukonde uliwonse, kuphimbira ziwaya ziŵiri zija za ku kunsonga kwa makapotolosi okhala pamwamba nsanamira zija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi makangaza mazana anai a maukonde awiriwa; mizere iwiri ya makangaza ya ukonde uliwonse, akukuta zikho ziwiri za mitu, inali pa nsanamirazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
makangadza 400 a maukonde awiri okongoletserawo (mizere iwiri ya makangadza pa ukonde uliwonse, kukongoletsa mbale za mitu yapamwamba pa nsanamira);
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi makangaza mazana anai a maukonde awiri wa; mizere iwiri ya makangaza ya ukonde uli wonse, akukuta zikho ziwiri za mitu, inali pa nsanamirazo.