2 Chronicles 4:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiponso adatsiriza maphaka ndi mbiya zokhala pa maphakawo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapanganso maphaka, napanga mbiya zaphwamphwa khumi pamwamba pa maphaka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
miyendo pamodzi ndi mabeseni ake;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapanganso maphaka, napanga mbiya zamphwamphwa khumi pamwamba pa maphaka;