2 Chronicles 4:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Solomoni adapangitsa zinthu zimenezo zochuluka kwambiri, kotero kuti kulemera kwa mkuŵawo sikudadziŵike ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Solomoni anazipanga zipangizo izi zonse zochulukadi, pakuti kulemera kwake kwa mkuwa sikunayeseka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zinthu zonse zimene Solomoni anapanga zinali zochuluka kwambiri kotero kuti kulemera kwa mkuwa sikunadziwike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Solomo anazipanga zipangizo izi zonse zocurukadi, pakuti kulemera kwace kwa mkuwa sikunayeseka.