2 Chronicles 4:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoikaponyale pamodzi ndi nyale zake za golide weniweni, kuti ziziyaka m'kati mwenimweni mwa malo opatulika, monga kudaalembedwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zoikapo nyali ndi nyali zake za golide woona, zakuunikira monga mwa chilangizo chake chakuno cha chipinda chamkati;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zoyikapo nyale zagolide ndi nyale zake zagolide weniweni, kuti ziziyaka mʼkati mwenimweni mwa malo opatulika monga analembera,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi zoikapo nyali ndi nyali zace za golidi woona, zakuunikira monga mwa cilangizo cace cakuno ca moneneramo;