2 Chronicles 4:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adapanga zoikapo nyale khumi zagolide monga momwe kudaalembedwera, ndipo adaziika m'Nyumba ya Chauta, zisanu kumwera, zisanu zina kumpoto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga zoikapo nyali khumi zagolide, monga mwa ziweruzo chake; naziika m'Kachisi, zisanu ku dzanja lamanja, ndi zisanu ku dzanja lamanzere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Solomoni anapanga zoyikapo nyale khumi zagolide monga momwe kunalembedwera ndipo anaziyika mʼNyumba ya Mulungu, zisanu mbali ya kummwera, ndi zisanu mbali ya kumpoto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga zoikapo nyali khumi zagolidi, monga mwa ciweruzo cace; naziika m'Kacisi, zisanu ku dzanja lamanja, ndi zisanu ku dzanja lamanzere.