2 Chronicles 4:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanganso matebulo khumi, ndipo adaŵaika m'Nyumba ya Chauta, asanu kumwera, asanu ena kumpoto. Ndipo adapanga mabeseni agolide okwanira 100.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapanganso magome khumi, nawaika m'Kachisi, asanu ku dzanja lamanja, ndi asanu ku dzanja lamanzere. Napanga mbale zowazira zana limodzi zagolide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapanga matebulo khumi ndipo anawayika mʼNyumba ya Mulungu, asanu mbali ya kummwera ndi asanu mbali ya kumpoto. Iye anapanganso mabeseni agolide okwanira 100.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapanganso magome khumi, nawaika m'Kacisi, asanu ku dzanja lamanja, ndi asanu ku dzanja lamanzere. Napanga mbale zowazira zana limodzi zagolidi.