2 Chronicles 4:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanga bwalo la ansembe, bwalo lalikulu, ndiponso zitseko za bwalo, nazikuta ndi mkuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamanganso bwalo la ansembe, ndi bwalo lalikulu, ndi zitseko za kubwalo, nakuta zitseko zake ndi mkuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapanga bwalo la ansembe, bwalo lalikulu ndi zitseko za bwalolo ndipo anakuta zitsekozo ndi mkuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamanganso bwalo la ansembe, ndi bwalo lalikuru, ndi zitseko za kubwalo, nakuta zitseko zace ndi mkuwa.