2 Chronicles 6:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Inu Chauta, Mulungu wanga imvani pemphero la ine mtumiki wanu ndi kupemba kwanga. Mverani kulira kwanga ndiponso pemphero limene ine, mtumiki wanu ndikupemphera pamaso panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana chitero, labadirani pemphero la kapolo wanu, ndi pembedzero lake, Yehova Mulungu wanga, kumvera kufuula ndi kupempha kwake, kumene kapolo wanu apempha pamaso panu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Yehova, Mulungu wanga, imvani pemphero ndi pembedzero la mtumiki wanu. Imvani kulira ndi pemphero la mtumiki wanu limene ndikupempha pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana citero, labadirani pemphero la kapolo wanu, ndi pembedzero lace, Yehova Mulungu wanga, kumvera kupfuula ndi kupempha kwace, kumene kapolo wanu apempha pamaso panu;