2 Chronicles 6:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono munthu akachimwira mnzake, nauzidwa kuti alumbire, akabwera kudzalumbira patsogolo pa guwa lanu m'Nyumba muno,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akachimwira mnansi wake, ndipo akamuikira lumbiro lakumlumbiritsa, ndipo akadzalumbira ku guwa lanu la nsembe, m'nyumba yino;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Munthu akalakwira mnzake, nawuzidwa kuti alumbire, akabwera kudzalumbira patsogolo pa guwa lansembe la Nyumba ino,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akacimwira mnansi wace, ndipo akamuikira lumbiro lakumlumbiritsa, ndipo akadzalumbira ku guwa lanu la nsembe, m'nyumba yino;