2 Chronicles 6:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthuwo azikuopani ndi kumayenda m'njira zanu masiku onse a moyo wao pomakhala m'dziko limene Inu mudapatsa makolo athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti aope Inu kuyenda m'njira zanu masiku onse akukhala iwo m'dziko limene munapatsa makolo athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
motero iwo adzakuopani ndipo adzayenda mʼnjira zanu masiku onse amene adzakhale mʼdziko limene munalipereka kwa makolo athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti aope Inu, kuyenda m'njira zanu masiku onse akukhala iwo m'dziko limene munapatsa makolo athu.