2 Chronicles 6:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mwina anthuwo adzakuchimwirani, poti palibe munthu amene sachimwa, ndiye Inuyo nkudzaŵakwiyira ndi kuŵapereka kwa adani, kuti aŵatenge ukapolo kupita nawo ku dziko lakutali kapena lakufupi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akachimwira Inu (pakuti palibe munthu wosachimwa), nimukakwiya nao, ndi kuwapereka kwa adani, kuti awatenge andende kunka nao ku dziko lakutali, kapena lapafupi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pamene achimwira inu, pakuti palibe amene sachimwa, ndipo inu mwawakwiyira ndi kuwapereka kwa adani awo, amene awatenga ukapolo ku dziko lawo lakutali kapena pafupi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akacimwira Inu (pakuti palibe munthu wosacimwa), nimukakwiya nao, ndi kuwapereka kwa adani, kuti awatenge andende kumka nao ku dziko lakutali, kapena lapafupi;