2 Chronicles 6:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mfumuyo idati, “Atamandike Chauta, Mulungu wa Aisraele, amene wachitadi ndi dzanja lake zimene adaalonjeza ndi pakamwa pake kwa Davide bambo wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Alemekezedwe Yehova Mulungu wa Israele, wakunena m'kamwa mwake ndi Davide atate wanga, nakwaniritsa ndi manja ake, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo inati, “Atamandike Yehova, Mulungu wa Israeli amene wachita ndi dzanja lake zimene analonjeza ndi pakamwa pake kwa Davide abambo anga. Pakuti Iye anati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iye, Alemekezedwe Yehova Mulungu wa Israyeli, wakunena m'kamwa mwace ndi Davide atate wanga, nakwaniritsa: ndi manja ace, ndi kuti,