2 Chronicles 6:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mumtima mwake bambo wanga Davide ankaganiza zoti amange nyumba yomveketsa dzina la Chauta, Mulungu wa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide atate wanga anafuna mumtima mwake kumangira dzina la Yehova Mulungu wa Israele nyumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Abambo anga Davide anali ndi maganizo mu mtima mwawo oti amangire Nyumba Yehova Mulungu wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide atate wanga anafuna mumtima mwace kumangira dzina la Yehova Mulungu wa Israyeli nyumba.