2 Chronicles 6:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chautayo adauza Davide bambo wanga kuti, ‘Popeza unkaganiza mumtima mwako zoti undimangire nyumba, udachita bwino kumaganiza zimenezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova anati kwa Davide atate wanga, Popeza unafuna mumtima mwako kulimangira dzina langa nyumba, unachita bwino kuti unatero mumtima mwako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova ananena kwa abambo anga Davide kuti, ‘Popeza zinali mu mtima mwako kumangira Nyumba dzina langa, unachita bwino kukhala ndi maganizo amenewa mu mtima mwakomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova anati kwa Davide atate wanga, Popeza unafuna mumtima mwako kulimangira dzina langa nyumba, unacita bwino kuti unatero mumtima mwako;