2 Chronicles 6:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe si ndiwe udzamange nyumbayo, koma mwana wako wamwamuna amene udzabale, ndiye amene adzandimangire nyumba yomveketsa dzina langa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma sudzandimangira nyumba ndiwe, koma mwana wako wakudzatuluka m'chuuno mwako, iyeyo adzalimangira dzina langa nyumbayi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu si iwe amene udzamanga Nyumba ya Mulungu koma mwana wako, mwana amene iwe udzabereke. Iyeyo ndiye amene adzandimangire Nyumba.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma sudzandimangira nyumba ndiwe, koma mwana wako wakudzaturuka m'cuuno mwako, Iyeyo adzalimangira dzina langa nyumbayi.