2 Chronicles 7:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikatseka kumwamba kuti mvula isagwe, kapena ndikalamula dzombe kuti liwononge zomera zapadziko, kapena ndikatumiza mliri pakati pa anthu anga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikatseka kumwamba kuti pasakhale mvula, kapena ndikalamulira dzombe lithe za padziko, kapena ndikatumiza mliri mwa anthu anga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine ndikatseka kumwamba kuti mvula isagwe, kapena kulamulira dzombe kuti liwononge dziko, kapena kutumiza mliri pakati pa anthu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikatseka kumwamba kuti pasakhale mvula, kapena ndikalamulira dzombe lithe za padziko, kapena ndikatumiza mliri mwa anthu anga;