2 Chronicles 8:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntchito yomanga Nyumba ya Chauta ndi nyumba ya mfumu idamtengera Solomoni zaka makumi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m'mene Solomoni anamanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba yakeyake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patatha zaka makumi awiri, ndiye nthawi imene Solomoni anamanga Nyumba ya Mulungu ndi nyumba yake yaufumu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m'mene anamanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba yace yace,