2 Chronicles 8:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo anthu sadapatukepo pa zimene mfumu idaalamula ansembe ndi Alevi, zokhudza zinthu zonsezi ndiponso zokhudza nyumba zosungiramo chuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sanapatuke pa lamulo la mfumu la kwa ansembe ndi Alevi, kunena za kanthu kalikonse, kapena za chumachi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu sanapatukepo pa zimene mfumu inalamula ansembe kapena Alevi pa china chilichonse, kuphatikiza za chuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sanapambuka pa lamulo la mfumu la kwa ansembe ndi Alevi, kunena za kanthu kali konse, kapena za cumaci.